menu Home chevron_right

Prince Mw Baby

South Africa [Malawian]

Biography


Dzina Langa ndine PRINCE M BANDAH wa Zaka 30, Ndimachokera mu Boma la Mangochi T/A Mponda ,mmudzi wa manjawira mu Banja la a Seleman Masamba,ndine oyamba Ku badwa mu banjali mwa ana 6.Pano ndili Mu Republic of South Africa.Sukulu ndaphunzira pa Mbonechera Primary, high school ndaphunzira pa Thumu Community day secondary.Ndinayamba kuyimba ndili ndi dzaka 12 , Ngati Ku school mumadziwa zija zoyimba nkalasi ,Ndasogolerapo nyimbo pa church Ngati nkristu,zonsezi zimatheka chifukwa ndimatha kulemba nkhani nkuyipanga nyimbo pompo pompo.Nde chifukwa cha luso limemeli Ndinali munthu mmodzi okonda kuyimba nyimbo nkusatila oyimba apa Malawi ,Mmodzi mwa iwo amame amandisangalatsa ndi Fredokis ndi Lady pace nsikana wa Ku mzudzu nyimbo zawo nkamamvera zimandisangalatsa mpaka zimandipasa masonphenya olowa Studio,Koma kamba ka mavuto Aza Chuma zimandivuta ,Mu 2019 mpamene ndinazaonekera poyera ndi Lutso Langa mu Banana Bush records ndi nyimbo Za chikondi,Ndimayimba Trap ,Chifukwa chokumana ndi oyimba osiyana Aiyana komanso kumva malangizo awo mmayimbidwe ,ndasankha kulangidza nane Dziko Langa Kuzera mmayimbidwe ,Dzina lomwe ndimagwilitsa ntchito Ngati Stage Name ndi __ Prince mw Baby ,Ena Amati PRINCE BABY .Koma mu nyimbo zanga Logo Yanga Ndi Prince Malawi baby. Ndikukusimikizirani Kuti ndabwera ndi Nkhokwe ya nyimbo Za chikondi Ndithu,Ndipo nyimbo zanga mu zikonda.


Social profiles


Booking contacts

Agency: Mrise

Phone: +27 67 386 1528

Website: www.malawirise.com

Email: support@malawirise.com


 • Search for: Songs, Artists…. etc
 • Thumbnail
  1 Tracks | 2020
  Thumbnail
  1 Tracks | 2020
  1 Tracks | 1970
  Thumbnail
  Adzatimenyera Nkhondo
  1 Tracks | 2020BOOKING CONTACT


  • cover play_circle_filled

   01. Zimangochitika(Prod. Womta)
   Chillz X K Laxce X Womta X Maujer

   file_download
  • cover play_circle_filled

   Rise Shine show
   Rise Shine show

  play_arrow skip_previous skip_next volume_down
  playlist_play